Advent Yohane Mogesi

Advent Yohane Mogesi Proclaiming the Advent of Jesus Christ

19/06/2023

Osaiwala kupanga like page yangai for more encouraging and teaching words.

19/06/2023

NDIMAKONDA NTHANOYI

translation sir yohane mogesi
Source; moffat wakalumpha mogesis post

Mwanyamuka kapu(chikho) yakuofi, nde mwagundana ndimunthu mkutayana khofiyo paliponse.

Mchifukwa chani wataya khofi?
Chifukwa wins wake wandigunda.

Yankho lolakwika

Mwataya khofi chifukwa ndamene anali mumkapumo,mukanakhala tiyi mukanataya tiyiyo.zomwe zinali mumkapumo ndizomwe zinakatayika.

Nde moyo ukavuta mkukugwedezani zomwe zili mwainu ndizomwe zidzatuluke, zingatheke kuzibisa km zikafikapo zidzatuluka, nde tizifuse tokha kt zli mwaine mchani? Pamene moyo wanyansa zidzatuluke mchani?

Kpn ndichisangalaro, mpamvu, mtendele ndi kupilira?

Mkwiyo, kuwawidwa, mau aukali, ndikubwelera mmbuyo.

Moyo umapeleka kapu ndipo Inu mumassnkha zoikamo.

Lero tiyeni tiyesele kudzadzitsa makapu athu ndichimwemwe, kukhululuka, kusangalala, mau achilimbikitso, kukoma mtima, kudekha ndi chikondi chapaena.♥️♥️♥️♥️

22/04/2023

CHARITY DEEDS.
We are working to help those that are jobless by giving them talents, the works we have began with is bricklaying(construction) and tailoring. For people and groups interested should contact the director, PHILADELPHIA SHOPS AND SCHOOLS +265 887515656 calls only what's up+265 889900306, we also work with primary schools to help those children that are less privileged, if you are interested visit us, OUR CHALLENGES, we are not helping others because we have plenty no! But because we also care about others we are not working for any benefits since then our great challenge is materials to provide those we have teach the works, and materials to make uniforms for school children, HOW CAN I TRUST FB GROUP PHILADELPHIA? Anyone willing to help should come and follow up our acts and choose those to help i.e own it own you can visit acertain school and call us to work uniforms for 50 students and prove that we have gave the uniforms to u, to those learning brick laying and tailoring we release application and the applied person's should be reconsidered by both the well-wishers and we and you help them. At last may God bless achearfuigiver.

Address

Chilimba
Blantyre

Telephone

+265883884987

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Advent Yohane Mogesi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share


Other Performance & Event Venues in Blantyre

Show All