DJ Slayder ozephy

DJ Slayder ozephy Private Dj

03/10/2022

Ex kunditumizila chithuz ali ndi new boyfriend wake, ine ndangopanga forward kwamene amamulipilira fees akhaule

01/10/2022

Komaso osamakakamiza ubale, kuliso Yesu kuseliku akufuna iwe

16/09/2022

Free Fredokiss
Sanalakwe
Zangovuta
K*t
Chilungamo
Chimawawa

13/09/2022

Jay Jay Cee Mw. Supala

13/09/2022

unabwela kudzakhala

13/09/2022

Ndika votera Phyzix ndiwa humble komaso amandimenyelabho

13/09/2022

bhobho koma

13/09/2022

Ma celebrate nthawi yakwana
Mutilambile kkkk
Achina charisma

Koma Gwamba anabweladi Pangani muwonele zimenezi
26/07/2022

Koma Gwamba anabweladi
Pangani muwonele zimenezi

AKUMUWONA MARTSE APA NDANI?
19/05/2022

AKUMUWONA MARTSE APA NDANI?

18/05/2022

Reply to 🇲🇼 🇲🇼

30/04/2022

zaidzeefran's short video with ♬ original sound

03/03/2022

RUSSIA YATULUTSA SITIMA YAKE YOOPSA KWAMBIRI YOTCHEDWA 'TYPHOON'

Sitima yoopsa kwambiri padziko lonse yotchedwa 'Submarine Typhoon' yatulutsidwa.

Sitimayi ndiya dziko la Russia ndipo mwa zina ili ndikuthekera komila m'madzi ndikuyenda pansi pa nyanja kwa masiku 120.

Sitimayi ndiyayitali ma metre 175 ndipo imasungila ma bomba 24 amphavu kwambiri oti akhoza kuononga theka la Europe mu mphindi zochepa.

Anthu ogwila ntchito okwanila 160 ndi omwe amafunikila kuti Sitimayi igwile ntchito yake pa Madzi.

Sitimayi yakhala ikusungidwa ku 'Reserve' kwa nthawi yayitali koma yatulutsidwa pa nthawi yomwe Russia ikulimbana ndi Ukraine.

-Naomi Kamiza



20/02/2022

- DJ LOMWE
- TANAPOSI
-TWINZA
-YOUNG K asanasinthe NAME
-BIRIWIRI
-YOUNG LOVE
-JUDA GAGA
-PHYZO NOT Phyzix
-GWAMBA wakale makamaka ija ya ndidikika
- Achina AB
-THIRD EYE
-EMOTIONS
-SONYE
-Truemale
-FREDOKISS WAKALE
-JB

Nyimbo za madolo amenewa ndimazimvelabe ndipo sizimandikwana

28/01/2022

KODI
Ku
BBC
LERO
MWAFIKAKO
?

11/01/2022

Everything Entertaining, Informing and Educating Check News and Download Songs, From www.adzukulu.com

SOBER SOBER
13/12/2021

SOBER SOBER

Address

Chiradzulu
Chiradzulu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Slayder ozephy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to DJ Slayder ozephy:

Share

Category


Other Chiradzulu event planning services

Show All