World Music

World Music Telling the people about music industry

07/07/2023

Video ilibwino koma audio mbola tibwelere nkati

Manong'ono akutero kuseliku

๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ

Bundle manja as we're waiting for the big tune from our brothersNo therapy by Veda njuchi & charisma madness๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ Pa...
20/11/2022

Bundle manja as we're waiting for the big tune from our brothers

No therapy by Veda njuchi & charisma madness

๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ Pamtsetse komaso mofaya agwire ntchito yake ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

Sanalekelere ndipo anati ndiyese mwayi
20/11/2022

Sanalekelere ndipo anati ndiyese mwayi

06/09/2022

We're back again ๐Ÿ˜…

Osamayima ngati mkazi watani kodi iweAnthu ma group akung'ung'udza ndi pause ya phyzix ๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ
29/04/2022

Osamayima ngati mkazi watani kodi iwe

Anthu ma group akung'ung'udza ndi pause ya phyzix ๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ

Connection fee yanga inee ๐Ÿ™†๐Ÿ™†๐Ÿ™†๐Ÿ™†
22/04/2022

Connection fee yanga inee ๐Ÿ™†๐Ÿ™†๐Ÿ™†๐Ÿ™†

Congratulations ๐ŸŽ‰๐Ÿ‘ Jay Jay Cee for being a leader of mabilinganya empireBwalo ndilosiirana pamene Mary P AKA Don GoGo  a...
20/04/2022

Congratulations ๐ŸŽ‰๐Ÿ‘ Jay Jay Cee for being a leader of mabilinganya empire

Bwalo ndilosiirana pamene Mary P AKA Don GoGo akutura pasi udindo ndipamene Jay Jay Cee akukhara father was group la mabilinganya empire

anthu maso alipaiwe kuti uwabweretsera zotani

Once again congrats ๐ŸŽ‰

Congratulations Leslie Bee jay zavuta zitayang'ana chidodo a Bee Jay chakupweketsaniDJ nyimbooo ikhare
17/04/2022

Congratulations Leslie

Bee jay zavuta zitayang'ana chidodo a Bee Jay chakupweketsani

DJ nyimbooo ikhare

Some other men are wick ๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ
08/04/2022

Some other men are wick ๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ

Judgement Day ๐Ÿšถ๐Ÿšถ
01/04/2022

Judgement Day ๐Ÿšถ๐Ÿšถ

Zinthu zikusinthadi ndaonaso ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿƒ
04/03/2022

Zinthu zikusinthadi ndaonaso ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿƒ

๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ My country people
08/02/2022

๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿšถ๐Ÿšถ๐Ÿšถ My country people

Ukwati uliko mawa๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚Ndimawu ati akuyankhulidwa apa??
26/11/2021

Ukwati uliko mawa๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Ndimawu ati akuyankhulidwa apa??

22/11/2021

Akufusa achimwene akulu uku๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Ukali wako
22/11/2021

Ukali wako

Once again ๐Ÿ™

Happy birthday chichewa Landlord Pitiliza kutipasira chichewa chothyakuka pa mpanje pano๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ
04/11/2021

Happy birthday chichewa Landlord

Pitiliza kutipasira chichewa chothyakuka pa mpanje pano๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

Kod za Top shella kwanuko zilipatiKunotu iliku mortuary ayipha anyamatawaLike th e page for more information
03/11/2021

Kod za Top shella kwanuko zilipati

Kunotu iliku mortuary ayipha anyamatawa

Like th e page for more information

 Akutulusa nyimbo yake lero pa made on Monday Like the page for more updates ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ
06/09/2021



Akutulusa nyimbo yake lero pa made on Monday

Like the page for more updates

๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

04/09/2021

Chonde abale ndi anasi musamutalikire Ekcess komwe aliko tingave zina mawa linoo

๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿƒ

04/09/2021

Bola ukamwera mowa

Oyimba kuchulutsa kuzipopa koma alibe kalikose๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Kumeneku timati kuphushaaaOsamangokalira wakuti ndiwakuti dolo mndani ayi
27/08/2021

Kumeneku timati kuphushaaa

Osamangokalira wakuti ndiwakuti dolo mndani ayi

MALAWI NA TANZANIA :- STEVE SPESHO PRODUCES FOR HARMONIZE ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ

Tanzania's Multi award winning star, Harmonize is ready and set to release a new single 'TEACHER' today at 10am produced by Steve Spesho ๐Ÿ‘๐Ÿ‘

Are you ready?????????
19/08/2021

Are you ready?????????

๐Ÿ’ฅ๐Ÿ’ฏHello Fam here is an artwork of a New track Dropping this coming monday & it ll' be primierd on made on monday
Help to spread the News

Nkhani yavuta ma group 6th ndi yoooo or badman chabe???Osaiwara kupanga like and share
19/08/2021

Nkhani yavuta ma group 6th ndi yoooo or badman chabe???

Osaiwara kupanga like and share

25/05/2020

Mwadzuka bwanji atsikana amene mumagona ziboda m'mwamba ngati mukubereka chosecho mwangokwatiwa kumene

Ulemu wanu๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

``Kago ulikuti ndikumalize" Ndinyimbo iti imakusangalatsani ya Ka-Sir blanca ChargieKa-Sir blanca ChargieKa-Sir blanca C...
06/04/2020

``Kago ulikuti ndikumalize"

Ndinyimbo iti imakusangalatsani ya Ka-Sir blanca ChargieKa-Sir blanca ChargieKa-Sir blanca Chargie blanca Chargie

03/09/2019

**** Mafana zakale ziiwaleni ku killer kapena Kuphedwa pa beat ase ziiwalen

Helloo Malawi the track you have been waiting for will be dropped very soon be ready



BY

MAKATA X SPARK X KCY

BOOM

26/08/2019

Hello Malawi

Tidziwitsanepo ziwiri zitatu nyimbo mwakhara mukuyiyembekezera from ikutuluka pompano akuti hardcore dancehall osati njenjede zikuveka mmafoni mwanuzi ayi be ready for this track

21/08/2019

Kunali ill elements, Don dada alliance and nyasa guruzi pano alikuti???

Oho ndeuzidziwa kuti naweso uzapita komwe aliko 1 day

20/08/2019

Hello Malawi

You have been waiting for so long a biggest hit song by our own artists

Dj wimbe X 6th X Tay guy_ wine up

And now the song is out. You can download it on www.entertainment.com the links will be dropped so soon

Thank you

With the widest selection of premium savings available, Entertainmentยฎ Members experience more for less. We create valuable connections between consumers, business partners and communities.

Address

Post Office 28
Kasungu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when World Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share


Other Performance & Event Venues in Kasungu

Show All