DjNoxy Mw

DjNoxy Mw Music 🎶 mixing up 🇲🇼

23/11/2024

😂Chiko ku Lilongwe

23/11/2024

Chikweza chi mbongo

16/11/2024

Shayaaa🤧😂😂😂

😂
16/11/2024

😂

Sakuyankha phone Ali ndi akazi ameneyo

Lilongwe yatenga
15/11/2024

Lilongwe yatenga

BLANTYRE VS LILONGWE LIVE MIC BATTLE

Pa nthawi imene tinkachititsa Mic Battle anthu ambiri a ku Blantyre omwe amamukonda Jasamah akhala akumachita matama kumati kumalawi kuno sikuzapezekanso oimba ok*tha ma freestyle kuposa Jasamah Nyasi M'maso

Izi anthu a ku Lilongwe sizinawamvekere bwino pak*ti kumenekoso kuli wawo emwe amamuti LORD GAGA ameneso anthu a ku Lilongwe amakhulupilira k*ti Jasamah sangadyemo ndipo ali k*tali kwambiri chabe sanayambepo wapasidwa mpata k*ti dziko limudziwe bwinobwino koma oyankhulawo akhala akumati Jasamah amayenda mbali tsiku ndi limodzi azakumane ndi LORD GAGA ndipomwe atazasiye zibwana

Zonsezi mene zimachitika pali organizer wina amangoyang'ana kufikila week ino wapanga organize show yomwe itakhale ku NDIRANDE CHIFUNDO HALL ndipo waitanisa anthu awiriwa k*ti akamenye Mic Battle ndipo akaoneke Dolo k*ti ndi ndani?

Funso mkumati Kodi amene mumamudziwa Lord GAGA Kodi ndiwoopsyadi mok*ti Jasamah udolo onse ukathera pompo?

Iyiyi ndi Lilongwe Vs Blantyre this coming Sunday Dolo akaoneke🙌

GIG 🇲🇼🖤
29/08/2024

GIG 🇲🇼🖤

23/08/2024

Mutipempheleko ku boma njuga ya betpawa achotse ku Malawi kuno azibambo ambili akusokonekera makukamu💔🤲plz chonde 🙄

🇲🇼🚶

23/08/2024

Tsogolo lili ngati kumaliseche aliyense amasukako Yekha 🙄🤔😂🙌

🇲🇼🚶

23/08/2024

chitseko chaku bank kaya
Chimadziwa bwanji k*ti uyu
Ndimoya moya ndimuonetse
Kiyama!🙄🤔
Nanji ku NBS 🚶

Good music to people 🇲🇼🤲
23/08/2024

Good music to people 🇲🇼🤲

🇲🇼wozza lah Friday ⌛
23/08/2024

🇲🇼wozza lah Friday ⌛

23/08/2024

Heartbreak mpaka kukanika kubiba😭😭😭😭🥺💔

28/07/2024

Kupanga tikupanga km kufunika inu k*t mutitenge🇲🇼🎧
In progress booking

Morning fam🇲🇼🤎Hardwokr don't give up Pa Lilongwe boma 🌅Nanga nthawi yonseyi🇲🇼🎧Komas ma link tiponyelen✊
17/07/2024

Morning fam🇲🇼🤎
Hardwokr don't give up
Pa Lilongwe boma 🌅
Nanga nthawi yonseyi🇲🇼🎧
Komas ma link tiponyelen✊

✋😝elis Lazaro AbwEzI njuchi ziwili😂🙌
17/07/2024

✋😝elis Lazaro AbwEzI njuchi ziwili😂🙌

Kunalibe ma cartoon kapena ma phone k*ti useweletsa game basitu masewela anali amenewa

Address


Telephone

+265884429423

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DjNoxy Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to DjNoxy Mw:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Event Planning Service?

Share