DJ Uncle Wiz

DJ Uncle Wiz Club DJ

11/11/2023

Hit after hit mix with DJ Uncle Wiz ๐Ÿ”ฅ
Are you ready!!! ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

Inna Lillahi wa inna ilayhi raji'unRest in peace brother.
08/10/2023

Inna Lillahi wa inna ilayhi raji'un
Rest in peace brother.

07/10/2023

4th November Robins Park Pamodzi Album Launch ๐Ÿ”ฅ
Jay Jay Cee Mw

26/08/2023

koma Man U si team wamba๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

16/06/2023

In all situations, God is in control.

22/05/2023

ELI Njuchi Yabaya ๐ŸŽถ ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

09/05/2023

Walelo
Real Madrid straight win.... ๐Ÿ”ฅ

07/05/2023

Eeh atipweteka

07/05/2023

Yasala ya Man United ๐Ÿ›‘
We go again.

07/05/2023

Kuswa kuswa ma Bankers ๐Ÿ’™๐Ÿ’™

FULL TIME

Ekwendeni 1-3 Silver

06/05/2023

Good morning beautiful people.

28/03/2023

Azipita kwawo.

27/03/2023

Who is your favorite singer, and what is the name of the song which you like the most?

08/03/2023

Happy women's day to all women's across the world ๐ŸŒŽ

08/02/2023

Enanu mpaka lero simuziwa Tathauzo la VN ngati mumaliziwa tanenani kuti ndichani ?? ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

27/01/2023

๐Ÿ˜‚MKALASI ILIYONSE SIMULEPHERA๐Ÿ˜ฒ
1. Mwana wamfupi wanzeru
2. Mnyamata okonda kujambula
3. Atsikana atatu oyenda limodzi okondedwa ndi aphunzitsi
4. Mnyamata wokonda kubwera mochedwa
5. Mnyamata wooneka bwino ofunidwa ndi atsikana
6. Mtsikana wokongola zedi wofunidwa ndi anyamata
7. Chimnyamata chamwano choti chimayankha aphunzitsi
8. Wakuba
9. Wanthabwala
10. Kagulu ka atsikana amiseche koma sikakhonzaso bwino
11. Mnyamata wamakani
12. Mnyamata wotchuka ndi mpira
13. Anyamata okhala kumbuyo koma osokosa zedi
14. Mtsikana wamatama osacheza ndi anzake
15. Mnyamata wandewu
16. Mnyamata wokonda kuthawira
17. Mwana wokonda kujombajomba
18. Mwana wodwaladwala
19. Kagulu kokonda mtsutso
Iwe udali gulu liti????????????

Happy New Year!
01/01/2023

Happy New Year!

24/11/2022

World Cup ipweteka anthu iyi.

03/11/2022

He's Dead But His Music ls Still Alive
Guess the Artist ๐ŸŽถ

02/10/2022

Mpaka 4 kwa duuu ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Kale lathu , ana enanu musanabadwe ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
25/09/2022

Kale lathu , ana enanu musanabadwe ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Let's support our very own gospel artist ....?
23/09/2022

Let's support our very own gospel artist ....?

08/09/2022

MALAWI Walelo 101:

1= Kumeneko akuyaka?๐Ÿ˜ช

2= Lero akutuluka?๐Ÿ’ง

3= Akuthira pati?โ›ฝ

4= Lero ayima pati?๐Ÿšจ

5= Ndidyapo zingat?๐Ÿ˜‚

FTMalawi 6-0 ComorosTabitha Chawinga scored a hat trick and voted player of the match.This was her last game as she will...
05/09/2022

FT

Malawi 6-0 Comoros

Tabitha Chawinga scored a hat trick and voted player of the match.
This was her last game as she will be leaving tomorrow for Inter Milan.

Wishing you all the best Captain.
Katundu wa boma

03/09/2022

Tamia ja wapepesa kwa Waxy Kay.

02/09/2022

AKUMANDIKOMORA
Alangizi apa page lino tandithandizeniko chonde ineyo ndili ndi chibwenzi ndie mamunayo anamudalitsa ndi chida cha bambo chachitali zedi komanso chonenepa. takhala pa ubwenzi kwa zaka ziwiri ndipo tayamba zogonana chaka chinochi.
sindine virgin koma tsiku loyamba kugona nae ndinabanika kwambili mpaka ndinakomoka koma iye anapitiliza mpaka kuthira komweku .
adandipepesa kuti mwina ine ndine virgin nane ndinangovomera kuti eyadi ndinali virgin mwina ndichifukwa chake. mwenzi watha tinapanganso ndipo ndinakomokanso. tapanga kokwana katatu ndipo maulendo onsewa ndikumakomoka coz chikumakagunda penapake pomwe ndikumabanika mpaka kukomoka.
kotelo ndinayanba kumuthawathawa kumupanga ignore kuti chibwenzi chingotha kozi ndikuopa andipweteka koma iye atazindikira kuti ndayamba kumuthawa dzulo anatengana ndi amalume ake ndi achimwene ake kubwera kwathu kudzafunsira banja. ine ndinathawako mpaka lero sindinapite kunyumba ndagona kwa agogo anga.
kodi ndikapita kunyumba ndikawauze chani makolo anga. ndikavomere banjalo kapena nkawafotokozere mai anga kuti banja ndakana coz mamunayu amandikomola ndi chida chake chachikulu.
help me chonde ndie kuti kubanjako ndizikakhalira kukomoka nayo game kapena ndingokana za banjazo kapena mwina chikazolowela kulowa ndidzasiya kukomokako.
musandigende chonde
Odandaula
Mzimba

โšฝ๏ธ SuperSportโšฝ๏ธ Cape Town Cityโšฝ๏ธ SwallowsGabadinho Mhango has scored in three successive games for AmaZulu FC  ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ
20/08/2022

โšฝ๏ธ SuperSport
โšฝ๏ธ Cape Town City
โšฝ๏ธ Swallows
Gabadinho Mhango has scored in three successive games for AmaZulu FC ๐Ÿ”ฅ ๐Ÿ”ฅ

16/08/2022

2 games 2 goals
Gabadinho Mhango uja ndi machine.

Premier League Race Has Started ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
15/08/2022

Premier League Race Has Started ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

13/08/2022

Walelo Blantyre Derby.

Mighty Mukuru Wanderers FC vs Nyasa Big Bullets

Your prediction?

13/08/2022

Two causes of heart diseases
ยถ falling in love
ยถ being Man United fan

Zina umangowona waziyamba ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚
13/08/2022

Zina umangowona waziyamba ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

12/08/2022

Alipo amene adayamba kucheza ndimunthu pa fb then kukumana physically mpaka banja?

Ziliko ๐Ÿ™Œ
10/08/2022

Ziliko ๐Ÿ™Œ

09/08/2022

Azimayi akapsa mtima amatha kumakauza kamwana ka miyezi itatu anvekere "Bambo anutu akupezerani mayanu ena mh ndipo azimayiwa mm "๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ’”

06/08/2022

Ambiri ang'amba ma ticket ah Liverpool ๐Ÿšฎ

Former Malawi national goalkeeper Mc millan Kishombe has died this morning at his home village Kayuni in Karonga.May his...
03/08/2022

Former Malawi national goalkeeper Mc millan Kishombe has died this morning at his home village Kayuni in Karonga.
May his soul rest in peace.

02/08/2022

The only way to find peace about your future is by trusting that God is bigger than your worry and entirely capable of guiding you.

Address

Area 36
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Uncle Wiz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share

Category

Nearby event planning services


Other DJs in Lilongwe

Show All