Chriss 1997

Chriss 1997 Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chriss 1997, Performance & Event Venue, Phalombe.

16/07/2024

Ngati tili mmatsiku osiliza ndiye malawi ili pa no 1.

16/07/2024

Kodi bakili muluzi tv siinatuluse VD ina?

15/07/2024

Kabambe akusewela ndale zamasana ena ali maso tuzuuuu akuona.

30/06/2024

Aliyense angoti ndilibe lawyer.

Muzabwele kumalawi mudzatiphunzise opposition ya nyoo.
26/06/2024

Muzabwele kumalawi mudzatiphunzise opposition ya nyoo.

25/06/2024

Pamene a digree akusowa ntchito anthu opanda digree ali pa ntchito osaziwanso ntchito nkomwe, nde malawi ameneyo.

24/06/2024

Pamene tikuganiza zokagona ena akukapanga ndale, ndale sachita masana.

Ichi sichinangogwa ulele chili ndi zosatila zake.
24/06/2024

Ichi sichinangogwa ulele chili ndi zosatila zake.

22/06/2024

Let's welcome the new followers Chrispin Mtambalika, Muhammad Wisick Zein, Maxwell Phwazo

16/06/2024

Iyaa bola Namalomba ife tikalankhula athana nafe.

14/06/2024

Asilikali amene akhala akukambidwa ku bakili muluzi tv aja adya sache on the same day by comrade Ntanyiwa.

14/06/2024

Freedom is coming tomorrow

14/06/2024

Ine chisoni chinayambira patali abale athu anakhapidwa pa mbowe palibe chachitika mpaka pano, ojiya ena ndi kumati akhapana okhaokha eeeee misonzi siikutha mmmm

14/06/2024

Even yesu anati musandililire ine koma muzililire nokha.

13/06/2024

Night mare

13/06/2024

Tikakhala ife misonzi siikutha mpaka pano kuyambila pomwe munatilanda boma lomwe limamva madando athu.

12/06/2024

Ndale sapanga masana

12/06/2024

Israel mmmmmm

Address

Phalombe
PHALOMBEZONE

Telephone

+265885865893

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chriss 1997 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share