Tsar-Ahamadu Patriotic Shamuzy Constantin Online

  • Home
  • Tsar-Ahamadu Patriotic Shamuzy Constantin Online

Tsar-Ahamadu Patriotic Shamuzy Constantin Online Typically Replies Instantly On Crucial Matters!!

Mwana wa khoswe mmodzi aposa mikango chikwi yomwe ndi yakufa. Mkazi waulemu ndi wodziwa ntchito ndinso udindo wake aposa...
12/07/2023

Mwana wa khoswe mmodzi aposa mikango chikwi yomwe ndi yakufa.
Mkazi waulemu ndi wodziwa ntchito ndinso udindo wake aposa mkazi wokongoletsa mmaonekedwe yemwe salemekeza mwamuna wake komanso thupi lake. Kudya phala losapsa mulibe nkwawa kuposera kundya mpunga wanyama muli mu chitsime cha nkwawa. Kugwa BP kaamba kakuduka kwa headset mkomveka kusiyana ndi kugwa BP chifukwa cha zochitika zamunthu yemwe mwakumana okulakula.🏋️🏋️

12/07/2023

Munthu wina adali kuweta nyama zak*tchire zosiyanasiyana munkhalango yake. Patsiku losegulira nkhalangoyi k*ti anthu atha kumakaona nyama zosiyanasiyana,adauza khwimbi la anthu lomwe lidasonkhana pafupi ndi chipata cha game reserve'yo kufka pafupi ndi polowera nkhalangoyik*ti ofuna kulowa munkhalango no alipire ndalamazi yokwana K5000.00,koma palibe analogies. Mwini nkhalangoyik*ti adaziwa nyengo mpaka kufika pa k750.00 koma palibe amene anampasa khobidi. Kenaka mwini nkhalango ija adauza anthu k*ti alowe munkhalangomo osalipira kalikonse ndipo mosataya nthawi,anthu onse aja adalowa munkhalango ndi msangala😃.Zitatero mwini nkhalangoyo adatseka chipata (gate) nakasegulira nyama zamitundu inali yolusa ndipo anawauza anthuwo k*ti yemwe alipire ndalamazi yokwana K20,000.00 ndiyemwe amusegulire k*ti apulumuke kumaona azilombozo. Atate to,anthu onse adali pakalpakala kuli pita mkumatuluka mu game uja.

PHUNZIRO
Pali anthu ena amene amafuna awonesese zomwe timakwanisa ndi mmene timachitira. Mwayi wotero ukapezekatiyeni tiwaonetse zomwe timuthandize kuposera angamati year opusa yamoto waeif🙏

⚠️STOP GBV!Ingomusiya apite mwamtendere akakumane ndi anthu ena omwe azizawafotokozera za kuipa kwako. Zabwino zako saza...
12/07/2023

⚠️STOP GBV!
Ingomusiya apite mwamtendere akakumane ndi anthu ena omwe azizawafotokozera za kuipa kwako. Zabwino zako sazazikamba mkomwe. Azakhala atapeza ma results a experiment yomwe amkachita koma mozondoka.

11/07/2023

She once said:
Am going to look for a caring husband,wandikwana🤗.
Her real friends encouraged her to force-prove my stupidity.
She started having private sexual affairs. She kept on doing whatever she could and she succeeded. Today she has all what she wanted. She was ineed serious.

07/07/2023

⚠️Anthu otsatirawa ndi amene amalankhula choona,koma nthawi sitimawakhulupirira popeza ndife anthu oziwa kuweruza mopanda mzeru:
📣Mwana
📣Munthu amene walezera
📣Munthu yomwe wapsa mtima

02/07/2023

Chikondi chokakamiza chili ngati kulowa mu nsapato yaing'ono😂. Ukalimbana nayo imatha kukhadzuka kapena kukupweteka phazi. Beware⚠️ ma yuthi mungazathere pachingwe⚰️ pazinthu zopeweka.
Vomerezani k*ti sinthawi yanu.

22/06/2023

When marriage ends, it brings internal peace and lesson learnt shapes ones future plans on how to handle some situations. Do not get depressed,accept the situation and move on.
Feedback:[email protected]

Mwamuna wankhanza sapezetsa mtendere. Mkadzi wosakhwima mzeru, amabweretsa mavuto pamoyo. Gwadani, pempherani. Anthu ote...
26/01/2023

Mwamuna wankhanza sapezetsa mtendere.
Mkadzi wosakhwima mzeru, amabweretsa mavuto pamoyo.
Gwadani, pempherani. Anthu otere, amavuta kusinthika. Mpempheni mbuye wanu k*ti akuchosereni mtundu wa chipsinjo chamtundu umenewu monga mmene muchitira pa chipsinjo chilichonse chokumana nawo. Pangatalike chotani, mbuye wanu azachotsa vutoli. Muzayamba kukhala mwamtendere ngakhale mulibe chakudya pakhomo panu. Madzi akumjigo owawa mchere omwewa, muzayamba kunenepa nawo. Mukazamayenda pamsewu, muzizaona zolowa ndi zotuluka. Musasowe mtendere ngati chala chogwidwa ndi nthenda ya katulutulu.
safe.
wize.

feedback: [email protected]

26/01/2023

OPITA KOSIYANA, SAPIKITSANA

Ena amatha kumapikitsana nawe iwe usakudziwa. Amayenda nawe ngati abale. Mkumatseka nawe ngati ndi mtendere. Kenako, amazichita associate kwa mkadzi wako kapena chibwenzi chako poti ena amaganizabe k*ti mwamuna pofokera pake ndi pa mzimayi. Amakhala pa mpikisano wazaoneni. iwe phee pa gear one, then mkuzapuma pa mtengo wa mango. iwo amazapuma pa road block during vehicle check. osamalimbana nawo, keep on doing what is best for you.
Kaya mzandale asiyeni azipanga.
Ali mu nthawi ya zinjoyi.
Bongololo sadzolera mafuta pagulu.
Dekhani.
Tiyeni tidekhe.😀😀😀😀😀😀😀😀😀😀

16/01/2023
08/01/2023

Ngati mungakhale ndi mtima woti musangalase aliyense, muzakhala kapolo wakaganizidwe. some people born to criticize, demote, devalue and dismay others. it is therefore better to stay alone, than being surrounded by fake people. Do not depend on someone. Be focused. Be safe. Be wise. Good sunday.

APM's guard commander in operation!!
13/10/2022

APM's guard commander in operation!!

Reference
13/10/2022

Reference

09/10/2022

Muzitha kuzipangitsa k*ti ena akuoneni ngati simungakwanitse kugula malaya eni eniwa;kufikira okuonani azaziwe k*ti ndi kuzindikira k*ti muli ndi kampani yopanga zovala.
.

09/10/2022

Moyo uli ngati bathing towel,malo amene wapuk*tira pa thako mmama, nthawi ina umazapuk*tira pakamwa! Aliyense amakhala ndi nthawi yake yofunika. Ajawa mumawati achambawa, azakhala pa forefront kukagula matabwa a deni yanu yomaliza. Azimayi mukuwati opeperawa,azayenda ndimapazi kuzungulira mudzi wonse k*tolera ufa ndi nkhuni k*ti ma contractor amene azakonze nyumba yanu azasuke mkamwa. Anzanu mukuwatamawo azafika pamaliro anu ndi mafoni akulu akulu ndinso ma bluetooth speaker. Atavala ma thirauza oboola ngati nyumba za mbira mitu iri pululuu ngati asekhwe. Mmalo mokulirirani azayamba kuweruza dera lakwanu k*ti ndikumatope. Misewu yake ndiyamagweru ngati mkamwa mwa mbuzi. Azalankhula ndi shoveli k*ti abanduke mwachangu asakafike ndi mdima. Apa mk*ti abusa omwe mukuwanyoza k*ti ndi akumuziwa atapasidwa ntchito yoikitsa chitanda chanu mu nthakaa. Musamasimbwe!!!

02/10/2022

i think pakhale malamulo apadera. Mkazi azipasidwe written permit k*t achape zovala za mwamuna wake coz mchitidwa woiwalira makondomu mmatumba a buluku ukuchulukirabe.🙈🙈🙈🙈🙈🙈

05/07/2022

Don't worry all of you!! I was involved in ICT refresher trainings. To be back soon!! Thanks for being observants!!

Address


Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Tsar-Ahamadu Patriotic Shamuzy Constantin Online posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Tsar-Ahamadu Patriotic Shamuzy Constantin Online:

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Event Planning Service?

Share