Nzeru entertainment Africa

Nzeru entertainment Africa � it's All � About � media�Zankati�mwandime�

22/08/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Evolisto Mw, Chisomo Culture Chiching, Frësh Nëyø, Mdala Zuze

A Very Big Loss For Malawi Music IndustryRest in Peace Andrew Masauli m'modzi mwa ma Twins odziwika bwino muno m'malawi ...
07/04/2023

A Very Big Loss For Malawi Music Industry

Rest in Peace Andrew Masauli m'modzi mwa ma Twins odziwika bwino muno m'malawi ndi maimbidwe monga "Ndizifinyika, Pasa ine, Single ndi nyimbo zina zambiri zomwe zinaimbidwa ndi anyamata amenewa otchedwa Twin-M

Wamwalira dzulo kuchipatala Cha Queen Elizabeth in Blantyre pamene wadwala mwa kanthawi chochepa ndipo mene amakafika kuchipatalako nkuti atatisiya kale

Andrew Masauli is From Blantyre, Baluti ndipo mwambo onse wa maliro udziwika a ku banja akalankhula

Just Like dis page for more info........

New music in town🔥🔥🔥🔥
05/04/2023

New music in town🔥🔥🔥🔥

20/11/2022
10/09/2022

CONDUCTOR🌬
PPiksyNdiwakuZomba ndipo sangakane.

🌬KUNOooo!!!🌪

Ngati sunamvele town monger sumvela made on monday any way dis truck it🔥APASENi💯
07/01/2022

Ngati sunamvele town monger sumvela made on monday any way dis truck it🔥APASENi💯

Address

Matawale
Zomba

Telephone

+265994564628

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nzeru entertainment Africa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share


Other Performance & Event Venues in Zomba

Show All