API ARTS

API ARTS Just for fun

03/12/2022

Tikusala ndi anthu 7 okha basi kuti tikwanise 1k downloads......
Kwa amene sitidapangebe download link nayi
(Share post if possible)
https://mdundo.com/song/2095277

Just for funy
06/04/2022

Just for funy

Just for fun😎
05/04/2022

Just for fun😎

05/04/2022
05/08/2020

PEPA MTIMA WANGA
Kandakatulo aka kangobadwa lero lomwe....kolakatulidwa ndi Andrew Pilliot
Khalani oyamba kuyimvera potumiza mawu oti *PMW* Ku whatsapp number iyi
+258 842 121 915 (osachotsera kapena kuonjezera number yo ilembeni mmene ilili chifukwa siya Ku Malawi) ndipo pompo pompo mukhala oyamba kuimvera
(Link ifika soon)

Titele
15/07/2020

Titele

Cash madam adatulutsa ka n**e dziko lidali chetechete......Lero Vube wabwera ndi yake koma sikutokota kwakeko..... Anywa...
21/06/2020

Cash madam adatulutsa ka n**e dziko lidali chetechete......
Lero Vube wabwera ndi yake koma sikutokota kwakeko.....

Anyway how many likes for Vube?

 Joy Nathu akukaikilidwa kuti ndi yemwe wapanga hack page ya abusa Che Wikise Baba
20/06/2020


Joy Nathu akukaikilidwa kuti ndi yemwe wapanga hack page ya abusa Che Wikise Baba

Chifukwa cha corona Black Nina wayamba yopenta nyumba
19/05/2020

Chifukwa cha corona Black Nina wayamba yopenta nyumba

Happy birthday
18/05/2020

Happy birthday

Chinga family or Moffat family?
17/05/2020

Chinga family or Moffat family?

*TATSITSA MITENGO YATHU*_malingana ndi mlili umene wagwedeza dziko lonse uwu wotchedwa Covid 19 *API ARTS* yatsitsa mite...
10/05/2020

*TATSITSA MITENGO YATHU*
_malingana ndi mlili umene wagwedeza dziko lonse uwu wotchedwa Covid 19 *API ARTS* yatsitsa mitengo motele_
👉```article:``` k500
👉```audio upload:``` k1200
👉```video upload:``` k1500
👉```YouTube chanel (create):``` k5000
👉```YouTube video upload:```k1500
👉```pdf upload:``` k500
👉```post booster:``` k15000 (for 5 days)
👉```page promoter:``` k15000 (for 5 days)
Tipezeni pa WhatsApp number iyi +258842121915 (osasintha kapena kuonjezera number yo)
Kapena pa
E-mail: [email protected]
Kapena pa
G-mail: [email protected]
Kapena pa
page yathu ya *API ARTS*
*API ARTS* [the home of arts]

Takumana ndi Sispence akupinyulisa keyboad 🏃🏻🏃🏻🏃🏻🏃🏻🏃🏻
10/05/2020

Takumana ndi Sispence akupinyulisa keyboad 🏃🏻🏃🏻🏃🏻🏃🏻🏃🏻

10/05/2020

Wikise once said......

100 likes yokha kwa Saint-Realest guys
10/05/2020

100 likes yokha kwa Saint-Realest guys

NDIUZE⏮◀⏸▶⏭Kodi nditadwala suzandithawa iwe?Nanga utandipatsa mimba suzaikana iwe?Mwamuna wanga mokupempha chonde ndiuze...
09/05/2020

NDIUZE
⏮◀⏸▶⏭
Kodi nditadwala suzandithawa iwe?
Nanga utandipatsa mimba suzaikana iwe?
Mwamuna wanga mokupempha chonde ndiuze
Kodi simudaimverebe ndakatuloyi?
Imvereni potsata link ili mmusiyo
Kapena lembani uthenga oti *NE* ku WhatsApp number iyi
+258842121915 (osaonjezera kapena kuchotsera number yo koma muilembe mmene ilili)
https://malawihits.com/andrew-pilliot-ndiuze-ndakatulo/

Download Andrew Pilliot - Ndiuze [Ndakatulo] on your favourite platform Malawi Hits!!!! Artist Na...

GWAMBA AGULA EP YA Taqwaa MW Pa mtengo wa 100 000 malawi kwacha
05/05/2020

GWAMBA AGULA EP YA Taqwaa MW Pa mtengo wa 100 000 malawi kwacha

DADADA or ADIDAS?
05/05/2020

DADADA or ADIDAS?

MKAZI WAKU TOWN..Kodi simudaimverebe?Tsatani link ili mmusiyi kuti mupange download.Kapena tumizani uthenga oti *MWT* ku...
03/05/2020

MKAZI WAKU TOWN..
Kodi simudaimverebe?
Tsatani link ili mmusiyi kuti mupange download.
Kapena tumizani uthenga oti *MWT* ku number iyi +258 842 121 915 (osachosera kapena kuonjezera number yo koma muilembe mmene ilili)
https://malawihits.com/andrew-pilliot-mkazi-wa-ku-town-ndakatulo/

Download this Poem by Andrew Pilliot called Mkazi Wa Ku Town on your favorite platform Malawi Hits. ...

Between A & B who is your best?Please like our page
01/05/2020

Between A & B who is your best?
Please like our page

Mongokukumbusani mix ndikale lija tinakuuzani 😬 tsiku lija nde ndimawa tiyeni tizaonere *Komwe Uliko* video song done by...
01/05/2020

Mongokukumbusani mix ndikale lija tinakuuzani 😬 tsiku lija nde ndimawa tiyeni tizaonere *Komwe Uliko* video song done by Mikhe Gee x Mista Kozmik (Shot By Kd) TV: MBC. Time : 6am to 7am. Program : GoodMorning Malawi. Host : Chisomo Manda 💯💥💥 Help us sharing the art FAM 🙏 kuyika olo pa status mukhala mutatidalitsa heavy 🎶
https://youtu.be/CTA8-uf7GCU

Copied from NamadingoNamadingoThe most frequent asked question on this page by some people is." KODI UNASIYA KUYIMBA ZAU...
30/04/2020

Copied from Namadingo
Namadingo

The most frequent asked question on this page by some people is.

" KODI UNASIYA KUYIMBA ZAUZIMU? " "ARE YOU A GOSPEL MUSICIAN?"

For the very last time The answer is " NO I am not a Gospel Musician. I am just
a Musician " It is my Job. I'm sure you also have jobs and they are not Gospel Jobs. I choose what to sing. The gospel is just another message I choose to share as I do my job. If you need a 100% Gospel Musician who only sings about Jesus in his Music then you have lots of them out there. I am not one of them. I also have other things I want to sing about. e.g Love. Education. Girls & Boys Empowerment. Wealth creation. Good morals. People and all that contributes to the well being of people in a society. If you are offended by such topics or u want a 100% gospel musician who mentions Jesus and God in every song he does. Then there are lots of them out there. I am not one of them. Make a screenshot. Tayankha Tayankha basi.

Note: kwaofuna mtsutso monga mwanthawi zambili. your comment will not get our reply on this.

Camera tatchera ku Phalombe📹📹📹📹📷📷📷📷Searching siginal......Anjira.......Follow API ARTS
29/04/2020

Camera tatchera ku Phalombe
📹📹📹📹📷📷📷📷
Searching siginal......
Anjira.......
Follow API ARTS

HAPPY  BIRTHDAY Thanzo MwWHO IS THANZO MW?Thanzo Mw is a Malawian upcoming RnB and Afro dance artist, based in Zomba. Th...
29/04/2020

HAPPY BIRTHDAY Thanzo Mw
WHO IS THANZO MW?
Thanzo Mw is a Malawian upcoming RnB and Afro dance artist, based in Zomba. Thanzo Mw is a stage name, his real real name is Frank T Joseph.
He begun dreaming of doing music right from primary school and the dream came into reality in 2017 where he realized his first track titled .
From there he has done several music featuring well known artists , Lady Temple, Cute M, Chrisgon, Starsha ,etc... Besides his achievements he's still dreaming in colours....
Here is one of his songs
https://www.mulanjemusic.com/builder/sites/www.mulanjemusic.com/medias/ndiwe-golide-by-thanzo-mw/
Please like this page

29/04/2020

ME: achina ujeni ku joniko simubwera?
UJENI: ndizabwera coronayi akatha.
.....coming soon!!!

Zoonesa maliseche zo  sizikutikhuza koma ife tingoti pitilizani kupanga suport oyimba akwathu kuno cash madam
29/04/2020

Zoonesa maliseche zo sizikutikhuza koma ife tingoti pitilizani kupanga suport oyimba akwathu kuno cash madam

Pakati pa MR JOKES ndi Gopani HenryWayaka moto ndi ndani pothyola sagwada za anthu ndi phwete?Please like our page
28/04/2020

Pakati pa MR JOKES ndi Gopani Henry
Wayaka moto ndi ndani pothyola sagwada za anthu ndi phwete?
Please like our page

Cash Madam koma mmene mukuonera mu industry ya music alimba?Dont forget to like our page
28/04/2020

Cash Madam koma mmene mukuonera mu industry ya music alimba?
Dont forget to like our page

Kwacha bwanji kumeneko?Here it is👇👇PiPiksyeat Ritaa-kuwawa......Za awiriwa mutiuze ndi inu ife tungofunapo nyimboyo 😎😎😎😎...
28/04/2020

Kwacha bwanji kumeneko?
Here it is
👇👇
PiPiksyeat Ritaa-kuwawa......
Za awiriwa mutiuze ndi inu ife tungofunapo nyimboyo 😎😎😎😎
🎵⏮◀⏸▶⏭
https://mikozinet.com/ritaa-x-piksy-kuwawa/

Endereço

Khongolote
Maputo

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando API ARTS publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Entre Em Contato Com O Negócio

Envie uma mensagem para API ARTS:

Compartilhar

Serviços De Planeamento De Eventos nas proximidades


Outra Serviço de festas e entretenimento em Maputo

Mostrar Todos