DJ Chibhwente

  • Home
  • DJ Chibhwente

DJ Chibhwente Truthful of Music
(2)

30/03/2024

Kale Kale anthu amayimba

Poti ma Show amatentha From Friday to Sunday. Nde nthawi yopita ku tchalitchi kapena ku Mzikiti  ikumapezeka koma? Kapen...
20/03/2024

Poti ma Show amatentha From Friday to Sunday. Nde nthawi yopita ku tchalitchi kapena ku Mzikiti ikumapezeka koma? Kapena Tchalitchi sichikapulumutsa munthu?

27/02/2024

Samala

24/02/2024

Pamene Ma prophet akugawa chimanga ma shehe m***a kumagawa ndiwo ntchitoyi ndiyothandizana Tiyeni tigwile popanda yankho.

TB: Interviews
15/02/2024

TB: Interviews

12/02/2024

Music Plug ✅
Coming Soon!!!!!!

11/02/2024

Osamapanga chibwana ndikumatchulamo Mulungu
Please ziwani ndi Mulungu olemekezeka ndipo ndiye akuwelengesa masiku a moyo wanu,Ndiye anakulengani yemweo anapanganso malekezelo a moyo wanu

RnB PakwaoTheo ThomsonX Bucci Worldwide
09/02/2024

RnB Pakwao
Theo ThomsonX Bucci Worldwide

Page Ikukanika kufika 10K IyiTiyeni mundikankhe abale anga ndinu nomwe.Pangani Post pa Wall panu Mundipange tag just to ...
08/02/2024

Page Ikukanika kufika 10K Iyi
Tiyeni mundikankhe abale anga ndinu nomwe.
Pangani Post pa Wall panu Mundipange tag just to get attention ya anthu

08/02/2024

Music Plug is A Beautiful Program than Born to Sing Malawi.

This Program is Improved from BTS I have Boosted the content from BTS and Decided to change the Name to
MusicPlug.
I know many Munandisika due to the break I had komano mukwelanso....

08/02/2024

I know Music....
I grew up listening to Different Genres
Of Music.
I don't Promote Music with only Money no
✅Money + Talents sound Good for me
>If one got Talent and got no money he is Good but turf to success for it.
Money is Good Yes
But for the love of Money many fall into Bad Temptations.
Music Plug..88%

😅😅😅
06/02/2024

😅😅😅

Munthu wakulakwilani chani uyu
26/01/2024

Munthu wakulakwilani chani uyu

Onsewa ali Single Ena ati ma Virgin ali pompoIf you have given a chance to marry one which one can be your Favorite Girl...
26/01/2024

Onsewa ali Single
Ena ati ma Virgin ali pompo
If you have given a chance to marry one which one can be your Favorite Girl🥰🥰🥰

How do you do at this point
23/01/2024

How do you do at this point

Zikuoneka kuti wapeza mkazi wachisilamu kumangochiko nde kaya!!! anthu ena akuganiza zoti ampangile mankhwala abwelele k...
23/01/2024

Zikuoneka kuti wapeza mkazi wachisilamu kumangochiko nde kaya!!!
anthu ena akuganiza zoti ampangile mankhwala abwelele kwao ku Phalombe.

His Journey is Over Rest in Peace Katelele!!!
18/01/2024

His Journey is Over
Rest in Peace Katelele!!!

10/01/2024

Chaka chino mawailesi ayamba kundiitana...................Nde Kaya mkupita kuti...Team Chibhwente

03/01/2024

Phwedo koma yeah

30/12/2023

Tangosowana Fadah

Pakuti pano Palibe mudzi okhalisaAheberi 14:13 Rest in Peace Akamwile
18/12/2023

Pakuti pano
Palibe mudzi okhalisa
Aheberi 14:13
Rest in Peace
Akamwile

Zithu Zimene sizimachitika chitika zikuchitika ku Phalombeku pa 26Ine ndi Djsavie Savie tingoyangana chifukwa nde kukuon...
13/12/2023

Zithu Zimene sizimachitika chitika zikuchitika ku Phalombeku pa 26
Ine ndi Djsavie Savie tingoyangana chifukwa nde kukuoneka kuti kukabebha ndithu 26 Dec A Place to Be!!!!!!

08/12/2023
06/12/2023

Mumuuze Namadingo tipange remix nyimbo ya Maury, nane ndili ndizoti ndilongosole 😅😅😅😅😅😅

28/11/2023

Gibo Pearson |
Slyc Amayenela award
Koma Easy.........

Mwana oti Ali ndi Luso uyuyu
25/11/2023

Mwana oti Ali ndi Luso uyuyu

Address


Telephone

0888566602

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Chibhwente posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to DJ Chibhwente:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Event Planning Service?

Share