Malawi Seventh-Day Adventist Music

Malawi Seventh-Day Adventist Music To advertise and promote about malawian good gospel music to the world
(2)

20/12/2024

Happy preparation day Agulu,
God bless you all.
Koma nyimbo ya Mpingwe Future Adventist Men titled "Abatizeni" mwaionela? Link in comment section

14/12/2024

Mwadzuka bwanji Agulu?
HAPPY SABBATH..

07/12/2024

Happy Sabbath Mpesa, have a blessed day...

06/12/2024

Kodi mwakonzeka (are you ready)?
HAPPY SABBATH AGULU...

06/12/2024

Happy preparation day Agulu, tukufunilani zabwino zonse..

30/11/2024

Happy Sabbath Agulu mukapembedza kuti anzathu? Have a wonderful day God bless you all...

29/11/2024

Happy Sabbath Mpesa, mwakonzeka?

29/11/2024

Happy preparation day Agulu mukhale ndi tsiku lopambana...

Lilongwe get ready chifukwatu Doris Kanyang'ama Chanza, akubwela kumeneko chakatu kukachimaliza ndimadalitso...
27/11/2024

Lilongwe get ready chifukwatu Doris Kanyang'ama Chanza, akubwela kumeneko chakatu kukachimaliza ndimadalitso...

Good morning  Agulu kwacha bwanji kwanuko komaso week mwaiyamba bwanji? Tamvani za nkhani ya Kabula Gospel Project, nang...
25/11/2024

Good morning Agulu kwacha bwanji kwanuko komaso week mwaiyamba bwanji? Tamvani za nkhani ya Kabula Gospel Project, nanga inu chaka chimalizeni ndi za Mulungu tachoka kutali....

23/11/2024

HAPPY SABBATH MPESA.
Mupita olo muli ndi zifukwa zokwanila?

22/11/2024

HAPPY SABBATH AGULU i hope you're all ready..

22/11/2024

Happy preparation day Agulu,
Kaya kwacha bwanji konse komwe muli?

Agulu aku Mangochi nawo sanawasiye kunja, onse omwe munkadandaula aja kuti kukhazikitsa chimbale cha PSALMS album by Pas...
18/11/2024

Agulu aku Mangochi nawo sanawasiye kunja, onse omwe munkadandaula aja kuti kukhazikitsa chimbale cha PSALMS album by Pastor Davie Chiwaya kwakuphonyani uwu ndi mwai wanu ku Mangochi ko kulengeza ndikomweku..

16/11/2024

Happy Sabbath Mpesa, mukapembedza kuti anzathu?

15/11/2024

Happy Sabbath Agulu,
mwakonzeka?

15/11/2024

Happy preparation day Agulu, all the best God bless you all...

13/11/2024

Aguĺu mulola kuti ukuku kukuphonyeni? Onalani video yi kuti mudziweko nokha..

Address

Seventh-Day Adventist Church
Blantyre

Telephone

+265992800187

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Seventh-Day Adventist Music posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share