Mwachidule JB wamukhulukira Lulu and Tygrin π mavete atalowa live Kwa 22mns amaliza motere
Kodi mwaimva? Tasenderani mumve nokha. Lulu & Mathumela Band akut sakumudziwa JB ndipo Ku southbend kuja sadakumameko nayoπ₯Ί
Mbali zakwanuko anti awa dzina lawo mumati ndani? Ife kwathu ndi Aunt Zayekha
Greater moments with the great Emcee
Happy Sunday to you all and have positive vibes every time... Identify the woman anaipatsa Motoπ₯
Lero tisaiwale timakhala ndi ma bundle keep on refreshing the page...π
Master of ceremony azibwera ndi vibe pamalo zimapereka chilimbikitso kut pamalopo Pakoma... Enjoy the arrival of Emcee Noah π€ in Mzuzu π₯π₯π₯π₯πππππ
Osaiwala kupephera chifukwa ena panopa akunenera dzina lanu kut zithu zisayende pa moyo wanu.
Ambuye akudalitseni pamene mukuyamba tsikuli.
Sample nyimbo za Gift ways as we are arranging to give you links and free few songs
#Advert#3
Kumbukirani kut mwambo wanu kuti zithuzi zizakhale zoneka bwino kufunika kupezaso garden yabwino with beautiful greenish areaβ»οΈππ
Mukufuna kupangitsa ukwati, chinkhoswe, bridal shower kapena send off?
Muli ndi misonkhano waukulu wa church koma malo anu akusowa? Muli ndi party ya birthday or yakuntchito?
#MM #Gardens ndi yankho la zonsezi. Located in Kasungu along Meru-Kasalika road.
Book your place with Mwawi Mkandawire on 0996885663 as spaces are very competitive
#beautifulgarden
##AffordableGarden