Kidd-Erraveda

Kidd-Erraveda Artist/Dj

15/09/2024

Who's a winner 🀐🀣

14/09/2024

TengeTenge naye aaa🀣

14/09/2024

Sho Madjozi
πŸ‡²πŸ‡Ό Ipase Moto freestyle πŸ”₯

With boysπŸ™πŸ—£οΈπŸ’™
14/09/2024

With boysπŸ™πŸ—£οΈπŸ’™

Let's go here I'mπŸ›€
14/09/2024

Let's go here I'mπŸ›€

14/09/2024

JETU ONLINE πŸ—£οΈπŸ‡²πŸ‡Ό

πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ’”
13/09/2024

πŸ€£πŸ€£πŸ€£πŸ’”

10/09/2024

Komatu MALAWI πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ’”

09/09/2024

With KWEMO – I just got recognized as one of their top fans!

Let's go πŸ”₯
03/09/2024

Let's go πŸ”₯

πŸ”₯
03/09/2024

πŸ”₯

https://ghettotunes.com/playback?a=I1vVPTYcZktEm_1641Let's download itπŸ€πŸ’–
25/08/2024

https://ghettotunes.com/playback?a=I1vVPTYcZktEm_1641
Let's download itπŸ€πŸ’–

Single . Other . Gang Ft. RashRock x Kid Erraveda by Fish Dee Fish Dee & Gang Ft. RashRock x Kid Erraveda Gang Ft. RashRock x Kid Erraveda AUDIO MP3 free DOWNLOAD. Recording Artists, Fish Dee on ghettotunes.com

🀣🀣🀣
10/04/2024

🀣🀣🀣

29/02/2024

Let's invite our friends to like this
Page 😍😍😍

25/01/2024

Kuwaona a Graduate πŸ’―βŒ

21/01/2024

Kineo Madness
πŸ”₯ more music fada

25/11/2023

Boma tsopano lavomereza kuti likutumiza achinyamata ku Israel kukagwira ntchito ya kuminda.

Boma lidatsutsa mphekesera imene imamveka kuti achinyamatawa akukamenya nkhondo ndipo kunyumba ya malamulo nduna za boma monga nduna yoona zakunja a Nancy Tembo komanso nduna yazamalonda a Sosten Gwengwe adatsutsa nkhaniyi mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma mnyumbayi a Kondwani Nankhumwa atafunsa za izi.

Ndipo mu chikalata chomwe wasayina ndi mlembi wamkulu ku unduna wa za ntchito a Wezi Kayira, boma lati achinyamatawa akukagwira ntchito mminda ndipo anyamuka nthawi iliyonse pa ulendo wa ku Israel.

Iwo ati anthu asadandaule chifukwa achinyamatawa akagwira ntchito malo otetezeka omwe angathe kukachotsedwako msanga ngati pangakhale zovuta.

A Kayira aonjezera kuti achinyamatawa adzikalandira ndalama ina yomwe adzikagwiritsa ntchito konko ndipo ina idzikaperekedwa ku ma account awo kuno ku mudzi, zimene ati zithandiza kuti dziko lino lidzipeza nawo ndalama yakunja.

Iwo ati iyi ndi ina mwanjira zomwe boma la a Lazarus Chakwera likuchita poonetsetsa kuti achinyamata akupeza ntchito.

Wolemba Cathy Maulidi

23/11/2023

Kineo Madness
πŸ”₯ weekend tulutsani
Trackiy

23/11/2023

Happy birthday LADY AIKA
πŸ‡πŸ‡

23/11/2023

Nasiya kuonera ma movie achimalawi zitheka bwanji mzimu kubwera utavala za DPPπŸ˜‚
Koma gyz

22/11/2023

Kwalero osapangako skip
Yankhulani Amen kwa
Mulungu πŸ™@

Address

Msundwe
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kidd-Erraveda posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share

Category


Other DJs in Lilongwe

Show All