Malawi music promo

Malawi music promo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi music promo, Sports Promoter, Mzuzu.

Abale Lay B Salima wayamba kuimba zichani izi?Atafunsidwa wayankha k*ti khumbo lake ndiloti abooleze Music industry ya k...
17/01/2025

Abale Lay B Salima wayamba kuimba zichani izi?

Atafunsidwa wayankha k*ti khumbo lake ndiloti abooleze Music industry ya ku Tanzania

Mwana uja wayamba kuimba chiswahiri zitithandiza izi? His now song called "BLAFU" Now Out

Mellz Kumpanje πŸ’ͺπŸ’₯
17/01/2025

Mellz Kumpanje πŸ’ͺπŸ’₯

Chomwe ndimaziwa ine ndi chak*ti "Munthu sumacheza wekha"...akulu akulu, uyu ndili naye pa chithunziyu ndi Bandera music ...ndipo ndikukhulupilira k*ti tonse Pano nkhani yake tikuidziwa...ndikunena Pano,adakali mmanja mwa a police akumusunga mchitokosi...fast fast forward, munthuyi akukanika k*tuluka kunali kuja chifukwa alibe lawyer omuthandizila k*ti nkhani ikambidwe imalizidwe k*ti atulukeko...nde ine ndili ndi mzanga lawyer amenenso ndi DJ, ndayesa kukamba naye... k*tengera ndi mmene ama chargila ma lawyer komanso poti ndiwaku Blantyre,Kwa ineyo ndikuona k*ti ndi fair price k*tengela ndi mtengowo, koma mwandekha ngati munthu sindingakwanise...wanena k*ti timupase MK650,000 mmalo mwa 1,000,000 pak*ti Bandera ndi munthu oti tonse Tili mu field imodzi...koma pamwamba pa 650 timuikilepo MK500,000 yamafuta yoyendera 3 hearings...imene tikawerengera ikukwana MK1,150,000....nde ndimati ndikupempheni mundithandize limodzi limodzi k*ti ndalamayi ikwane timutuluseko m'bale wathu uja ngati k*thekela k*telo muli nako...any amount will appreciated....Ayao amzanga tiliko Mesa??....

You can send through these accounts :

Airtel money : 0995072049 (Mellanie Joseph Msumba
Mpamba : 0885531911 (Kevin Chidothi)
National Bank : 1008151818

Ma transaction onse ndizaika pa page p***a muzaone...

Zikomo Mulungu akudalitseniπŸ™

14/01/2025

Morale the trapper mkana ntchulako ma artist angapo omwe akafuna kupakula and opakula wo ose mkanawa ntchula
Ife 500 pin tika wina ku bet tikukholan 🀣🀣🀣

The Martse Foundation has announced that the Martse Memorial Show will happen on 24th May, 2025
12/01/2025

The Martse Foundation has announced that the Martse Memorial Show will happen on 24th May, 2025

Eeish Afana Ceez πŸ”₯πŸ’―πŸ”₯  Anthu ochuluka atutumuka ndi oyimba Afana Ceez yemwe wapanga zinthu zachilendo pojambula nyimbo ya...
06/08/2024

Eeish Afana Ceez πŸ”₯πŸ’―πŸ”₯

Anthu ochuluka atutumuka ndi oyimba Afana Ceez yemwe wapanga zinthu zachilendo pojambula nyimbo yake yotchedwa PAKALA PAKALA galimoto lomwe amagwiritsa ntchito ya Gusheshe itanyamulidwa ndi Crane m'malere, ndipo ena ak*ti izizi zik*tanthauza k*ti music industry ikusintha ndipo oyimba ayamba kupanga zinthu zawo mwadongosolo, onerani nyimboyi pa link ili mmusiyi

https://youtu.be/uLBiaa5NdC8

28/07/2024

A Jolasto inuo mukusowatu bwa?

Jay Jay Cee Mw ft ELI Njuchi  awoDriemo handedeMZUZU MAFIA ft Nepman Link in comments section πŸ‘‡
24/07/2024

Jay Jay Cee Mw ft ELI Njuchi awo
Driemo handede
MZUZU MAFIA ft Nepman
Link in comments section πŸ‘‡

A ntondo Jay Jay Cee Mw walelo Walonjeza k*t pa 7 February ak*tulusa New music video. Nyimbo imozi mwa nyimbo zomwe zina...
03/02/2024

A ntondo Jay Jay Cee Mw walelo
Walonjeza k*t pa 7 February ak*tulusa New music video.
Nyimbo imozi mwa nyimbo zomwe zinali mu album yake
Video yomwe ak*tulusa pa 7 iyi title yake ndi nyimbo munaliso oyimba wina amene ndi Rashley Mw ife powona zimenezi tili okondwela chifukwa Jay Jay cee ndi munthu mozi mwama artist ozichepesa komaso olimbikila kupusha bgup fadahπŸ”₯πŸ’ͺπŸ™Œ

30/01/2024

Good morning family πŸ™πŸ™Œ

29/01/2024

Antondo Sherixtada Ick akufusa ak*ti kod bea wake akumulamulila ndinda?

Hala 0885084775 for upload and free promoπŸ™

Address

Mzuzu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi music promo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share